Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 4/06 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2006
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Tingachite Kuti Tikhale Osangalala
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Kodi Chimwemwe Chenicheni Chingapezeke Kuti?
    Nsanja ya Olonda—1997
  • Chimwemwe Chowona Potumikira Yehova
    Nsanja ya Olonda—1992
  • Kufunafuna Moyo Wachimwemwe
    Nsanja ya Olonda—2004
Onani Zambiri
Galamukani!—2006
g 4/06 tsamba 1-2

Zamkatimu

April 2006

Mungachipeze Bwanji?

Anthu ambiri amayesetsa kuti apeze chimwemwe, koma zimaoneka kuti ndi ochepa amene amachipeza. Chifukwa chiyani? Kodi chinsinsi chopezera chimwemwe chagona pati?

3 Mungathe Kupeza Chimwemwe Chenicheni

4 Njira Yopezera Chimwemwe Chenicheni

8 Kondwerani M’chiyembekezo

10 “Anaikidwa M’ndende Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo”

12 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Yesu Anaferadi Pamtanda?

17 Zimene Achinyamata Amadzifunsa

Kodi Kucheza ndi Anzanga a Ku Sukulu Kumapyola Malire Kukafika Pati?

20 Ndinaphunzira Kudalira Mulungu

29 Zochitika Padzikoli

30 Kuchokera kwa Owerenga

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Thandizo Poteteza Ana Athu

Ulendo wa Tsiku Limodzi wa ku Chernobyl 14

April ndi mwezi wokumbukira kuti patha zaka 20 chichitikireni ngozi yoopsa kwambiri ya nyukiliya yomwe inachitika panthawi yoti si yankhondo. Kodi anthu akupirira bwanji zotsatira za ngozi imeneyi?

Kulera Ana Omwe Amafunika Kuwamasalira Mwapadera 25

Anthu okwana atatu pa anthu 100 alionse padziko lapansi pano akuti ali ndi vuto linalake loganiza moperewera. Onani momwe mabanja akupiririra bwinobwino ngakhale kuti ali ndi ana amene ali ndi mavutowa.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena