Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 5/07 tsamba 28-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2007
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • ZINACHITIKIRA KUTI?
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 5/07 tsamba 28-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

ZINACHITIKIRA KUTI?

1. Kodi izi zinachitikira mu mzinda uti?

Lembani mzere wozungulira yankho lolondola pa mapupo.

Yopa

Yerusalemu

Asikeloni

Gaza

◆ Kodi Samsoni anapezeka bwanji m’kachisi wa Afilisti?

․․․․․

◆ N’chifukwa chiyani Samsoni anali ndi mphamvu zodabwitsa?

․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi nkhaniyi ikukuphunzitsani chiyani za Yehova?

ZINACHITIKA LITI?

Tchulani munthu kapena anthu amene analemba mabuku a m’Baibulo amene ali m’munsiwa ndipo lembani mzere kuchokera pa dzina la bukulo kufika pa chaka chimene bukulo linamalizidwa kulembedwa.

475 B.C.E. 455 B.C.E. 443 B.C.E. 60-61 C.E. 65-66 C.E.

2. Nehemiya

3. Estere

4. Aefeso

NDINE NDANI?

5. Ndinakana kuchoka paphwando ngakhale kuti mfumu inandiitana.

NDINE NDANI?

6. Paulo anapempha ineyo ndi Onesimo kuti tikapereke makalata ku Efeso ndi ku Kolose.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunsowa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo omwe akusowapo.

Tsamba 7 Kodi mphatso imodzi yochokera kwa Mulungu ndi iti? (Mlaliki 3:․․․)

Tsamba 10 Kodi Mulungu amawalonjeza zotani anthu osauka? (Salmo 9:․․․)

Tsamba 13 Kodi zabwino ndiponso zoipa zimachitika chifukwa chiyani? Tchulani chifukwa chimodzi. (Mlaliki 9:․․․)

Tsamba 19 Kodi n’chiyani chimene muyenera kuona mwa munthu amene mukuganizira zodzamanga naye banja? (1 Petulo 3:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungapeze zithunzi izi m’magazini ino? Fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali pa tsamba 28)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Gaza.—Oweruza 16:21-30.

◆ Samsoni anachita zinthu zomutayitsa mwayi wake wokhala Mnaziri.

◆ Yehova ndiye anam’patsa mphamvuzo.—Oweruza 16:28.

2. Nehemiya, pambuyo pa 443 B.C.E.

3. Moredekai, 475 B.C.E.

4. Paulo, 60-61 C.E.

5. Vasiti.—Estere 1:9-12.

6. Tukiko.—Aefeso 6:21, 22; Akolose 4:7-9.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena