Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 2/08 tsamba 1-3
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2008
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • Kukhala Bwinobwino M’chipale Chofewa 16
  • Nchifukwa Ninji Pali Upandu Wochulukira Chotero?
    Nsanja ya Olonda—1989
  • Pamene Kunalibe Upandu
    Galamukani!—1998
  • Kuyesayesa Kuthetsa Upandu
    Galamukani!—1996
  • Kodi Lili Kuti Dziko Lopanda Upandu?
    Galamukani!—1996
Onani Zambiri
Galamukani!—2008
g 2/08 tsamba 1-3

Zamkatimu

February 2008

Kodi Zachiwawa Zidzatha?

Anthu ambiri amangokhala mwamantha chifukwa cha zachiwawa zimene zikuchitika. Kodi pali njira iliyonse yothetsera zachiwawa zomwe zafala masiku anozi? Kapena tingoiwalako zoti vutoli lidzatha? Werengani zinthu zolimbikitsa zimene Baibulo limanena pankhaniyi.

3 Kodi Zachiwawa Zafika Poipa Zedi?

4 Kodi Zachiwawa Zingathetsedwe?

8 Posachedwapa Zachiwawa ‘Zidzatha’

10 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Mulungu Amakhululuka Machimo Akuluakulu?

12 Ndinali Mkulu wa Asilikali Koma Tsopano Ndine “Msilikali wa Khristu”

19 Kodi Mipukutu Yakale Inalembedwa Liti?

23 Inatenga Zaka Zoposa 120

29 Zochitika Padzikoli

30 Kuchokera kwa Owerenga

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Mphatso Yamtengo Wapatali

Kukhala Bwinobwino M’chipale Chofewa 16

Madera akumidzi okutidwa ndi chipale chofewa amaoneka ngati alibe zamoyo zilizonse. Komatu si choncho ayi.

Kodi Ndingatani Ngati Ndili ndi Matenda Aakulu Kapena Chilema? 26

Onani mmene achinyamata anayi akupiririra matenda aakulu ndiponso kulemala.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

Petrels: By courtesy of John R. Peiniger

[Mawu a Chithunzi patsamba 3]

Robson Fernandes/​Agencia Estado/​WpN

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena