Zamkatimu
October 2008
Ngati Mwana Wanu Amagwiritsa Ntchito Intaneti
Pamene mukuwerenga chiganizochi, ana mamiliyoni ambiri ali pa Intaneti. Kodi iwo akuchita chiyani pa Intanetipo? Kodi muyenera kuda nkhawa?
3 Kodi Mwana Wanu Amagwiritsa Ntchito Intaneti?
4 Ana Akamagwiritsa Ntchito Intaneti—Zimene Makolo Ayenera Kudziwa
8 Ana Akamagwiritsa Ntchito Intaneti—Zimene Makolo Angachite
10 Njati za ku Ulaya Zapulumuka Lokumbakumba
14 Puerto Rico—Dziko Lachuma M’dera Lotentha
22 Kumene Mtsinje Umayenda Cham’mbuyo
32 Aphunzitsi Ake Analiyamikira
Zizindikiro zimene Hillary anali nazo zinkasokoneza makolo ake. Kenako atakwanitsa zaka zisanu, vuto lake linadziwika.
Kodi Nthawi Yofikira Panyumba Ndiziiona Bwanji? 26
Dziwani zimene mungachite kuti muzitsatira nthawi yofikira panyumba imene makolo anu akuikirani.