Zamkatimu
January 2009
Madzi Akutha Padzikoli?
Chaka chilichonse anthu mamiliyoni ambiri amafa chifukwa cha uve komanso kumwa madzi oipa. Kodi pali njira iliyonse yothetsera vutoli?
3 Kodi Madzi Akutha Padzikoli?
5 Zimene Anthu Akuchita Pofuna Kuthetsa Vuto la Kusowa kwa Madzi
21 Anthu Otcheza Mchere ku Sahara
24 Akapolo Oiwalidwa a ku South Pacific
26 Anthu Ambiri Amakonda Pizza
32 Kodi Mulungu Amatisamaliradi
Kuthandiza Ana Amene Ali ndi Vuto Lophunzira 10
Kodi mungatani ngati mwana wanu ali ndi vuto lolephera kuwerenga kapena kuphunzira zinthu zina?
Kodi Tikamavutika Ndiye Kuti Mulungu Akutilanga? 28
Kodi mukamakumana ndi mavuto ndiye kuti Mulungu akunyansidwa nanu?
[Chithunzi patsamba 2]
Anthu akutunga madzi pa chitsime chachikulu, kutachitika chilala choopsa m’dera la Gujarat, ku India
[Mawu a Chithunzi]
REUTERS/Amit Dave