Zamkatimu
February 2010
Ngati Banja Silikuyenda Bwino Kodi Ndi Bwino Kungolithetsa?
Anthu ambiri akaona kuti banja lawo silikuyenda bwino, amathamangira zongolithetsa. Koma kodi imeneyi ndi njira yabwino yothetsera mavuto a m’banja? Kodi kuthetsa banja kumabweretsa mavuto otani? Nanga mungathetse bwanji mavuto a m’banja lanu popanda kuthetsa banjalo?
3 “Ndi Bwino Banja Lingotha Basi”
4 Zinthu Zinayi Zimene Muyenera Kudziwa Musanathetse Banja
8 Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Liyambenso Kuyenda Bwino?
10 Panagona Luso! Khungu la Shaki
11 Galamukani! Inathandiza Mayi Wina Kuti Asachotse Mimba
12 Zimene Baibulo Limanena Zoyenera Kuchita Mukakhala Pachibwenzi
14 Dzuwa Linafiira Ngati Magazi
16 Nankapakapa Ndi Mbalame Yokongola Kwambiri
26 Zimene Achinyamata Amadzifunsa N’chifukwa Chiyani Ndimangokhalira Kukangana ndi Makolo Anga?
32 “Ndikupempha Kuti Mundithandize”
Ndinali Msilikali Panopa Ndikutumikira Mulungu 18
Panthawi ya nkhondo yachiwiri ya padziko lonse, zinali zovuta kuti msilikali wa ku Germany wa m’gulu la SS, asamvere lamulo loperekedwa ndi akuluakulu a gululi. Koma msilikaliyu anachita zimenezi. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake anachita zimenezi.
Kodi Ndi Nzeru Kukhulupirira Mulungu? 22
Kodi mumakhulupirira kuti kuli Mulungu kapena ayi? Nkhaniyi ikuthandizani kudziwa zoyenera kukhulupirira.