Zamkatimu
September 2010
Kodi Mungatani Kuti Musamasungulumwe?
Kodi ndi zinthu ziti zimene zimachititsa kuti anthu azisungulumwa? Kodi mungatani kuti musamasungulumwe? Kodi anthu ena amachita zotani kuti asamasungulumwe?
3 Anthu Ambiri Amasungulumwa Ngakhale Kuti Pali Njira Zambiri Zolankhulirana
4 Kodi N’chiyani Chimayambitsa Kusungulumwa?
6 Zimene Mungachite Kuti Musamasungulumwe Kwambiri
16 Nyumba Zoyenda Nazo za Anthu a ku Asia
18 Chimtengo Chachikulu Chochokera ku Kanthanga Kakang’ono
19 “Mwina Nyimbo Ndi Imene Ingathandize”
24 Mfumu ya Nkhalango za ku America
32 Khalidwe Labwino Limene Aphunzitsi Amachita Nalo Chidwi
Ndinalowa Mpikisano Wabwino Kwambiri 12
Katswiri wina wothamanga wa ku Finland anaphunzira za mpikisano wopita ku moyo umene umatchulidwa m’Baibulo. Werengani nkhaniyi kuti mumve za chimwemwe chimene wapeza pamene akuyesetsa kuti adzapeze mphoto ya moyo.
Himogulobini Inapangidwa Mogometsa Kwambiri 26
Himogulobini ndi imene imachititsa kuti magazi azioneka ofiira. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake munthu sangakhale ndi moyo popanda himogulobini.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Published in Aamulehti 8/21/1979