Zamkatimu
February 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mungatani Kuti Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi?
TSAMBA 6 MPAKA 9
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YA
ACHINYAMATA
Mungapeze mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso ambiri amene achinyamata amadzifunsa. Nkhani zake ndi monga:
• “Kodi Ndimangokhalira Kuganizira za Maonekedwe Anga?”
• “Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula?”
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
ANA
Werengani nkhani zomwe zafotokozedwa pogwiritsa ntchito zithunzi. Gwiritsani ntchito nkhanizi kuthandiza ana anu kudziwa zambiri za anthu otchulidwa m’Baibulo komanso kuwathandiza kuti akhale ndi makhalidwe abwino.
(Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)