Zamkatimu
February 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mfundo za M’Baibulo N’zothandizabe Masiku Ano?
Mfundo Zake N’zothandiza Nthawi Zonse—Kuchita Zinthu Mwachilungamo
Mfundo Zake N’zothandiza Nthawi Zonse—Kusakwiya Msanga
Mfundo Zake N’zothandiza Nthawi Zonse—Kukhulupirika M’banja
Mfundo Zake N’zothandiza Nthawi Zonse—Chikondi
TSAMBA 3 MPAKA 7
MUNGAPEZENSO ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
MAVIDIYO AMAKATUNI
Onerani vidiyo yachingelezi yakuti, Be Social-Network Smart.
Gwiritsani ntchito Intaneti mosamala pamene mukucheza ndi anzanu.
(Fufuzani pa mawu akuti BIBLE TEACHINGS > TEENAGERS)
MAVIDIYO
Kupatsa n’kofunika kwambiri. M’vidiyoyi, onani mmene Kalebe ndi Sofiya akuphunzirira khalidweli.
(Pitani pamene palembedwa kuti BIBLE TEACHINGS > CHILDREN)