Zamkatimu
April 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MUNGAPEZENSO ZINTHU ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
NKHANI
Nkhaniyi ingakuthandizeni kuti muziganizira kaye mtundu wa magemuwo musanayambe kusewera. Ikuthandizaninso kuti muziganizira kuchuluka kwa nthawi yomwe mumawononga posewera magemuwa.
(Pitani pomwe alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
MAVIDIYO
Vidiyo ya ana imeneyi, ikusonyeza zimene zinathandiza Sofiya kudziwa zoyenera kuchita mchimwene wake akamulakwira.
(Pitani pomwe alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)