Mawu Oyamba
Zimatenga nthawi kuti munthu asiye zoipa zimene anazolowera n’kuyamba kuchita zabwino, koma kodi n’zothandiza?
Baibulo limati:
“Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake.”—Mlaliki 7:8.
Nkhanizi zili ndi mfundo za m’Baibulo zimene zingatithandize kuti tizolowere kuchita zinthu zabwino.