Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g20 No. 3 tsamba 16
  • Anasiya Tsankho

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anasiya Tsankho
  • Galamukani!—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Muzisonyeza Chikondi
    Galamukani!—2020
  • Mungapeze Thandizo
    Galamukani!—2020
  • “Mfundozi Zindithandiza Kwambiri”
    Galamukani!—2016
  • Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikhulupirira Kwambiri Mlengi
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Onani Zambiri
Galamukani!—2020
g20 No. 3 tsamba 16

Anasiya Tsankho

Onerani mavidiyo onena za anthu awa komanso ena ambiri pa jw.org.

Panopa amaonana ngati pachibale

Johny ndi Gideon akupereka moni kwa ana omwe ali panja ya Nyumba ya Ufumu ya Mboni za Yehova.

Ngakhale kuti poyamba anali osiyana mitundu komanso ankasiyana maganizo pandale, Johny ndi Gideon anayamba kugwirizana kwambiri.

Onererani vidiyo yakuti Johny ndi Gideon: Poyamba Anali Khoswe ndi Mphaka Koma Pano Ndi Ogwirizana. Fufuzani mutu umenewu pa jw.org.

“Ndinkafunitsitsa kuthana ndi kupanda chilungamo”

Rafika Morris.

Pofuna kuthana ndi vuto losankhana mitundu, Rafika analowa gulu la anthu ofuna kusintha zinthu. Koma atachita nawo msonkhano wachigawo wa Mboni za Yehova, anaona kuti wapeza mgwirizano womwe ankaufuna.

Onerani vidiyo yakuti Rafika Morris: Ndinkafunitsitsa Kuthana ndi Kupanda Chilungamo. Fufuzani mutu umenewu pa jw.org.

Anagonjetsa tsankho

Zithunzi: 1. Munthu wa Chiarabu ndi mnzake akuyenda kwinaku akucheza. 2. Munthu Wachiyuda akumwetulira akucheza ndi anzake.

Kodi n’chiyani chimene chinathandiza munthu wa Chiarabu komanso Myuda kusiya mtima watsankho?

Onerani vidiyo yakuti Kodi Chikondi Komanso Kukhulupirika Zidzagonjetsa Liti Chidani? Fufuzani mutu umenewu pa jw.org.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena