Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g22 No. 1 tsamba 3
  • Kodi Mungatani Kuti Mupirire Mavuto a M’Dzikoli?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungatani Kuti Mupirire Mavuto a M’Dzikoli?
  • Galamukani!—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Zili M’magaziniyi
    Galamukani!—2022
  • Kodi Mungatani Mutakumana Ndi Vuto Lalikulu?
    Galamukani!—2014
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
    Galamukani!—2022
  • 2 | Muzisamala Ndalama
    Galamukani!—2022
Onani Zambiri
Galamukani!—2022
g22 No. 1 tsamba 3
Mayi yemwe ali ndi nkhawa akuona pafoni yake zithunzi zosonyeza anthu akuchita zinthu zachiwawa, ngozi zam’chilengedwe, mayi wanyamula mwana wake, chithunzi cha pakompyuta cha kolonavairasi komanso chipatala.

Kodi Mungatani Kuti Mupirire Mavuto a M’dzikoli?

Kodi mumaona kuti panopa mukuvutika kwambiri ndi mavuto a m’dzikoli kusiyana ndi kale? Kodi mavuto otsatirawa amachitikanso kumene mukukhala?

  • nkhondo

  • miliri

  • ngozi zam’chilengedwe

  • umphawi

  • tsankho

  • uchigawenga

Zinthu zoopsa zikachitika, anthu ambiri amakhala ndi mantha komanso amakhala opanda chiyembekezo. Anthu ena akakumana ndi mavuto aakulu, amasokonezeka kwambiri. Komatu kusokonezeka kwambiri chonchi, komanso kukhala ndi mantha kwa nthawi yaitali kumangowonjezera mavutowo.

Mukakumana ndi mavuto, muyenera kuchita zinthu mwanzeru kuti muteteze okondedwa anu, thanzi lanu, ndalama zanu komanso zimene zimakuthandizani kuti mukhale osangalala.

Kodi mungatani panopa kuti mavuto obwera chifukwa cha zomwe zikuchitika m’dzikoli asamakukhudzeni kwambiri?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena