DZIWANI ZAMBIRI
Pitani pa jw.org ndipo fufuzani mutu wakuti, “Ntchito Komanso Ndalama.” Pa mutu umenewu mupeza nkhani zofufuzidwa bwino zomwe zathandiza anthu ambiri kuthana ndi mavuto awo. Zina mwa nkhani zimenezi ndi izi:
“Kodi Mungatani Kuti Musakhale Wokonda Ndalama?”
“Zimene Mungachite Ngati Mukupeza Ndalama Zochepa”
“Kodi Mungatani Kuti Muzigula Zinthu Mogwirizana Ndi Ndalama Zimene Mumapeza?”