Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g23 No. 1 tsamba 16
  • Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Zili M’magaziniyi
  • Galamukani!—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
    Galamukani!—2023
  • Mawu Oyamba
    Galamukani!—2023
  • Mulungu Akulonjeza Kuti Dzikoli Lidzakhalanso Bwino
    Galamukani!—2023
  • Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Galamukani!—2023
g23 No. 1 tsamba 16
Utsi woipa wochokera kumafakitale ukuwononga chilengedwe.

Xuanyu Han/Moment via Getty Images

Zimene Zili M’magaziniyi

Dzikoli lili pangozi.

Kodi likhalanso bwino kapena lizingoipiraipirabe mpaka kuwonongekeratu limodzi ndi zamoyo zonse? Werengani nkhani zimene zili m’magaziniyi kuti mudziwe zimene zikuchitikira dzikoli komanso ngati pali zifukwa zilizonse zotichititsa kukhala ndi chiyembekezo.

Kodi tsogolo la dzikoli ndi lotani pa nkhani ya:

  • Madzi abwino?

  • Nyanja zikuluzikulu?

  • Nkhalango?

  • Mpweya?

DZIWANI ZAMBIRI

Mzimayi akutenga Baibulo pashelefu.

Anthu ambiri amakhulupirira zimene Baibulo limalonjeza kuti tidzakhala ndi moyo wosangalala padzikoli mpaka kalekale. Onerani vidiyo yakuti Kodi Tingadziwe Bwanji Kuti Baibulo Limanena Zoona? pa jw.org.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena