Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • snnw tsamba 10
  • Kukonzekera Kupita Kolalikira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kukonzekera Kupita Kolalikira
  • Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Nkhani Yofanana
  • Kukonzekera Kupita Kokalalikira
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • “Ndine Pano! Munditumize Ine”
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Phunziro 3
    Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo
  • Timadzipereka
    Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onani Zambiri
Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
snnw tsamba 10

Nyimbo 145

Kukonzekera Kupita Kolalikira

(Yeremiya 1:17)

  1. Tsopano

    Kunja kwacha,

    Tikalalikiretu.

    Komano mvula,

    Yayambanso kugwa.

    N’zosavuta kupitiriza

    Kugona.

    (KOLASI)

    Tisafo’ke tikonzekere,

    Tipemphe Yehova,

    Iye angatilimbikitse

    N’zofunika.

    Tipezenso woyenda naye

    Wotilimbikitsa.

    Angelo angatithandize

    Osafo’ka.

  2. Chimwemwe

    Tidzapeza,

    Ngati sitingafo’ke.

    Ndipo Yehova

    Amaona zonse

    Sangaiwalenso chikondi

    chathuchi.

    (KOLASI)

    Tisafo’ke tikonzekere,

    Tipemphe Yehova,

    Iye angatilimbikitse

    N’zofunika.

    Tipezenso woyenda naye

    Wotilimbikitsa.

    Angelo angatithandize

    Osafo’ka.

(Onaninso Mlal. 11:4; Mat. 10:​5, 7; Luka 10:1; Tito 2:14.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena