Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • snnw tsamba 18-19
  • Kodi Mumamva Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mumamva Bwanji?
  • Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumamva Bwanji?
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nyimbo kwa Wammwambamwambayo
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga Khala Wanzeru”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • “Muzitha Kusankha Zinthu Zimene Ndi Zofunikadi Kwambiri”
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
snnw tsamba 18-19

Nyimbo 153

Kodi Mumamva Bwanji?

(Aheberi 13:15)

  1. Kodi m’mamva bwanji

    m’kazindikira kuti,

    mwasonyezadi khama

    pophunzitsa ena?

    Inde m’kayesetsa,

    M’lungu adzadalitsa.

    Mudzathandiza anthu

    kudziwa Mulungu.

    (KOLASI)

    Timasangalala ndithu

    kupereka mtima wathu.

    Choncho tim’tumikirebe

    tsiku lililonse.

  2. Kodi m’mamva bwanji

    m’kazindikira kuti,

    mwawafika pamtima

    akamva uthenga?

    Ena amakana,

    ena kunamizidwa.

    Koma timanyadira

    tikalalikira.

    (KOLASI)

    Timasangalala ndithu

    kupereka mtima wathu.

    Choncho tim’tumikirebe

    tsiku lililonse.

  3. Kodi m’mamva bwanji,

    m’kakumbukira kuti,

    mwa chikondi Yehova

    amatsogolera?

    Timalalikira,

    anthu timaphunzitsa,

    akhale ndi tsogolo

    adzapeze moyo.

    (KOLASI)

    Timasangalala ndithu

    kupereka mtima wathu.

    Choncho tim’tumikirebe

    tsiku lililonse.

(Onaninso Mac. 13:48; 1 Ates. 2:4; 1 Tim. 1:11.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena