Musaleke Kukwaniritsa Chilamulo cha Khristu
M’MAWA
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero
10:00 Kodi Chilamulo cha Khristu N’chiyani?
10:15 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu Ngakhale Pamene Anthu Ena Sakukuonani
10:30 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu Mukamalalikira
10:55 Nyimbo Na. 70 ndi Zilengezo
11:05 N’chifukwa Chiyani Tingati Chilamulo cha Khristu Ndi Chabwino Kwambiri?
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:05 Nyimbo Na. 51
MASANA
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 76
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu M’banja Lanu
2:30 Muzikwaniritsa Chilamulo cha Khristu Mukakhala Kusukulu
2:45 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo
2:55 Muzikondana Ngati Mmene Yesu Anakukonderani
3:55 Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero