Loweruka
“Nyadirani dzina lake loyera. Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale”—Salimo 105:3
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 53 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa
• Muzifunsa Mafunso (Yakobo 1:19)
• Muzigwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu (Aheberi 4:12)
• Muzigwiritsa Ntchito Mafanizo (Mateyu 13:34, 35)
• Muziphunzitsa ndi Mtima Wonse (Aroma 12:11)
• Muzisonyeza Kuti Mumawaganizira (1 Atesalonika 2:7, 8)
• Muziwafika Pamtima (Miyambo 3:1)
10:50 Nyimbo Na. 58 ndi Zilengezo
11:00 NKHANI YOSIYIRANA: Muzigwiritsa Ntchito Zomwe Yehova Watipatsa Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa
• Zinthu Zofufuzira (1 Akorinto 3:9; 2 Timoteyo 3:16, 17)
• Abale Athu (Aroma 16:3, 4; 1 Petulo 5:9)
• Pemphero (Salimo 127:1)
11:45 NKHANI YA UBATIZO: Mukabatizidwa Muzisangalala Kwambiri (Miyambo 11:24; Chivumbulutso 4:11)
12:15 Nyimbo Na. 79 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 76
1:50 Mmene Abale Athu Akusangalalira ndi Ntchito Yophunzitsa Anthu ku . . .
• Africa
• Asia
• Europe
• North America
• Oceania
• South America
2:35 NKHANI YOSIYIRANA: Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo . . .
• Kuti Azidzidyetsa Mwauzimu (Mateyu 5:3; Yohane 13:17)
• Kuti Azipezeka Pamisonkhano (Salimo 65:4)
• Kuti Asamacheze ndi Anthu Olakwika (Miyambo 13:20)
• Kuti Asiye Makhalidwe Oipa (Aefeso 4:22-24)
• Kuti Akhale pa Ubwenzi ndi Yehova (1 Yohane 4:8, 19)
3:30 Nyimbo Na. 110 ndi Zilengezo
3:40 VIDIYO: Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”—Mbali Yoyamba (Nehemiya 1:1–6:19)
4:15 Tikamaphunzitsa Anthu Tikukonzekera Kudzagwiranso Ntchitoyi M’dziko Latsopano (Yesaya 11:9; Machitidwe 24:15)
4:50 Nyimbo Na. 140 ndi Pemphero Lomaliza