Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CO-pgm19 tsamba 4-5
  • Loweruka

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Loweruka
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • MASANA
  • Loweruka
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2021
  • Loweruka
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2020
  • Lachisanu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019
  • Lachisanu
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2019
CO-pgm19 tsamba 4-5

Loweruka

“YENDANIBE M’CHIKONDI”​—AEFESO 5:2

M’MAWA

  • 9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 9:30 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero

  • 9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzisonyeza Chikondi Chosatha Mumpingo Wachikhristu

    • Muzikonda Amene Akutitsogolera (1 Atesalonika 5:12, 13)

    • Muzikonda Akazi Amasiye ndi Ana Amasiye (Yakobo 1:27)

    • Muzikonda Achikulire (Levitiko 19:32)

    • Muzikonda Amene Akuchita Utumiki wa Nthawi Zonse (1 Atesalonika 1:3)

    • Muzikonda Anthu Ochokera Kumayiko Ena (Levitiko 19:34; Aroma 15:7)

  • 10:50 Nyimbo Na. 58 ndi Zilengezo

  • 11:00 NKHANI YOSIYIRANA: Muzisonyeza Chikondi Chosatha mu Utumiki

    • Muzisonyeza Kuti Mumakonda Mulungu (1 Yohane 5:3)

    • “Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondera Wekha” (Mateyu 22:39)

    • Muzikonda Mawu a Yehova (Salimo 119:97; Mateyu 13:52)

  • 11:45 NKHANI YA UBATIZO: Phunzirani Kukonda Ena Kuchokera kwa Yesu (Mateyu 11:28-30)

  • 12:15 Nyimbo Na. 52 ndi Kupuma

MASANA

  • 1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo

  • 1:45 Nyimbo Na. 84

  • 1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Mmene Abale Athu Akusonyezera Chikondi Chimene Sichitha

    • Ku Africa (Genesis 16:13)

    • Ku Asia (Machitidwe 2:44)

    • Ku Europe (Yohane 4:35)

    • Ku North America (1 Akorinto 9:22)

    • Ku Oceania (Salimo 35:18)

    • Ku South America (Machitidwe 1:8)

  • 2:55 NKHANI YOSIYIRANA: Muzisonyeza Chikondi Chosatha M’banja

    • Muzikonda Mkazi Wanu (Aefeso 5:28, 29)

    • Muzikonda Mwamuna Wanu (Aefeso 5:33; 1 Petulo 3:1-6)

    • Muzikonda Ana Anu (Tito 2:4)

  • 3:35 Nyimbo Na. 35 ndi Zilengezo

  • 3:45 VIDIYO: Nkhani ya Yosiya Imatiphunzitsa Kukonda Yehova Komanso Kudana ndi Zoipa​—Mbali Yoyamba (2 Mbiri 33:10-24; 34:1, 2)

  • 4:15 Muziphunzitsa Ana Anu Mmene Angasonyezere Chikondi (2 Timoteyo 3:14, 15)

  • 4:50 Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero Lomaliza

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena