Lachisanu
“Tiwonjezereni chikhulupiriro”—Luka 17:5
M’MAWA
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: Kodi Chikhulupiriro Ndi Champhamvu Bwanji? (Mateyu 17:19, 20; Aheberi 11:1)
10:10 NKHANI YOSIYIRANA: N’chifukwa Chiyani Timakhulupirira . . .
• Kuti Mulungu Alipo? (Aefeso 2:1, 12; Aheberi 11:3)
• Mawu a Mulungu? (Yesaya 46:10)
• Mfundo za Makhalidwe Abwino za Mulungu? (Yesaya 48:17)
• Kuti Mulungu Amatikonda? (Yohane 6:44)
11:05 Nyimbo Na. 37 ndi Zilengezo
11:15 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: Nowa Anali Womvera Chifukwa cha Chikhulupiriro (Genesis 6:1–8:22; 9:8-16)
11:45 Muzikhala Ndi Chikhulupiriro Ndipo Musamakayikire (Mateyu 21:21, 22)
12:15 Nyimbo Na. 118 ndi Kupuma
MASANA
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 2
1:50 NKHANI YOSIYIRANA: Muzilimbitsa Chikhulupiriro Chanu Pogwiritsa Ntchito Zinthu za M’chilengedwe
• Nyenyezi (Yesaya 40:26)
• Nyanja (Salimo 93:4)
• Nkhalango (Salimo 37:10, 11, 29)
• Mphepo Komanso Madzi (Salimo 147:17, 18)
• Zolengedwa za M’madzi (Salimo 104:27, 28)
• Matupi Athu (Yesaya 33:24)
2:50 Nyimbo Na. 148 ndi Zilengezo
3:00 Ntchito Zamphamvu za Yehova Zimatichititsa Kukhala Ndi Chikhulupiriro (Yesaya 43:10; Aheberi 11:32-35)
3:20 NKHANI YOSIYIRANA: Muzitsanzira Anthu a Chikhulupiriro, Osati Opanda Chikhulupiriro
• Abele, Osati Kaini (Aheberi 11:4)
• Inoki, Osati Lameki (Aheberi 11:5)
• Nowa, Osati Anthu Ena a M’nthawi Yake (Aheberi 11:7)
• Mose, Osati Farao (Aheberi 11:24-26)
• Ophunzira a Yesu, Osati Afarisi (Machitidwe 5:29)
4:15 Kodi Mungatani Kuti ‘Mupitirize Kudziyesa Kuti Muone Ngati Mukadali Olimba M’chikhulupiriro’? (2 Akorinto 13:5, 11)
4:50 Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero Lomaliza