Limbitsani Chikhulupiriro Chanu!
M’MAWA
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero
10:00 N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kulimbitsa Chikhulupiriro Chathu Panopa?
10:15 Kodi Mumaona “Wosaonekayo”?
10:30 “Munthu Amakhala ndi Chikhulupiriro Chifukwa cha Zimene Wamva”
10:55 Nyimbo Na. 104 ndi Zilengezo
11:05 “Makhalidwe Amene Mzimu Woyera Umatulutsa Ndiwo . . . Chikhulupiriro”
11:35 Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa
12:05 Nyimbo Na. 50
MASANA
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 3
1:35 Zochitika pa Moyo Wachikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Nkhani Yosiyirana: Muzithandiza Ena Kukhala ndi Chikhulupiriro Cholimba
• Muzithandiza Ana Anu
• Muzithandiza Wophunzira Baibulo
• Muzithandiza Akhristu Anzanu
3:00 Nyimbo Na. 38 ndi Zilengezo
3:10 Tiziyang’anitsitsa “Mtumiki Wamkulu ndi Wokwaniritsa Chikhulupiriro Chathu”
3:55 Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero