Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • syr23 tsamba 2
  • Ziwerengero Zonse za 2023

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ziwerengero Zonse za 2023
  • Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Nkhani Yofanana
  • Ziwerengero Zonse za 2022
    Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2022 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziwerengero Zonse za 2024
    Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2024 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
  • Ziwerengero Zonse za 2017
    Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2017 la Mboni za Yehova
  • Ziwerengero Zonse za 2021
    Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
Onani Zambiri
Lipoti la Chaka cha Utumiki cha 2023 la Mboni za Yehova Padziko Lonse
syr23 tsamba 2

Ziwerengero Zonse za 2023

  • Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova: 85

  • Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 239

  • Mipingo Yonse: 118,177

  • Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 20,461,767

  • Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 22,312

  • Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikiraa: 8,816,562

  • Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,625,042

  • Kuwonjezereka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2022: 1.3

  • Obatizidwa Onseb: 269,517

  • Avereji ya Apainiyac Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,570,906

  • Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 738,457

  • Maola Onse Amene Tinalalikira: 1,791,490,713

  • Avereji ya Maphunziro a Baibulod Mwezi Uliwonse: 7,281,212

Chaka cha utumiki cha 2023 chinayambira pa 1 September 2022, ndipo chinatha pa 31 August 2023.

a Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?”

b Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?”

c Mpainiya ndi wa Mboni wobatizidwa komanso wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.

d Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa jw.org yakuti “Kodi Phunziro la Baibulo Lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?”

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena