Ziwerengero Zonse za 2024
Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova: 84
Mayiko Amene Anatumiza Lipoti: 240
Mipingo Yonse: 118,767
Opezeka pa Chikumbutso Padziko Lonse: 21,119,442
Amene Anadya Zizindikiro Padziko Lonse: 23,212
Ofalitsa Onse Amene Anagwira Ntchito Yolalikiraa: 9,043,460
Avereji ya Ofalitsa Amene Ankalalikira Mwezi Uliwonse: 8,828,124
Kuwonjezereka kwa Ofalitsa Kuchokera mu 2023: 2.4
Obatizidwa Onseb: 296,267
Avereji ya Apainiyac Okhazikika Mwezi Uliwonse: 1,679,026
Avereji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 867,502
Avereji ya Maphunziro a Baibulod Mwezi Uliwonse: 7,480,146
Chaka cha utumiki cha 2024 chinayambira pa 1 September 2023, ndipo chinatha pa 31 August 2024.
a Wofalitsa ndi munthu amene amalalikira mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengerochi, onani nkhani ya pa yakuti, “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?”
b Kuti mudziwe zimene mungachite kuti mubatizidwe n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani ya pa yakuti, “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?”
c Mpainiya ndi wa Mboni wobatizidwa komanso wachitsanzo chabwino amene amadzipereka kuti azilalikira uthenga wabwino kwa maola enaake mwezi uliwonse.
d Kuti mudziwe zambiri, onani nkhani ya pa yakuti, “Kodi Phunziro la Baibulo Lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?”