“Makhalidwe Anu Akhale Ogwirizana ndi Uthenga Wabwino”
M’mawa
9:40 Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero
10:00 Kodi Uthenga Wabwino Ukukuthandizani Kusintha?
10:15 Nkhani Yosiyirana: Mmene Uthenga Wabwino Unawathandizira
• Sitefano
• Filipo
• Akula ndi Purisila
• Tito
11:05 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo
11:15 Pitirizani ‘Kuchita Ntchito Zosonyeza Kuti Ndinu Odzipereka kwa Mulungu’
11:35 Nkhani ya Ubatizo: Pitirizani ‘Kugonjera Uthenga Wabwino’
12:05 Nyimbo Na. 37
Masana
1:20 Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero
1:35 Nkhani ya Onse: N’chifukwa Chiyani Mumakhulupirira Zimene Mumakhulupirira?
2:05 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:35 Nyimbo Na. 24 ndi Zilengezo
2:45 Nkhani Yosiyirana: “Tikusonyeza M’njira Iliyonse Kuti Ndife Atumiki a Mulungu . . . ”
• Popirira
• Pokhala Okoma Mtima
• Pochita Zinthu Moona Mtima
3:30 Kodi Uthenga Wabwino Umatiphunzitsa Chiyani?
4:00 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero