Mawu Oyamba
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi ndi ndani amene anatipatsa mphatso yabwino kwambiri kuposa zonse?
Baibulo limati: “Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba, pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo.”—Yakobo 1:17.
Nsanja ya Olonda iyi ikutithandiza kudziwa mphatso imene Mulungu watipatsa yomwe ndi yaikulu kuposa mphatso zonse.