CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NEHEMIYA 1-4
Nehemiya Ankakonda Kulambira Yehova
Losindikizidwa
455 B.C.E.
Nisan (Mar./Apr.)
2:4-6 Nehemiya anapempha chilolezo chomanganso Yerusalemu yemwe anali likulu la kulambira koona panthawiyo
Iyara
Sivani
Tamuzi (June/July)
2:11-15 Nehemiya anafika ku Yerusalemu panthawi imeneyi ndipo anayendera mpanda wa mzindawo
Aba (July/Aug.)
Eluli (Aug./Sept.)
6:15 Anamanga mpandawo masiku 52
Tishiri