CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NEHEMIYA 5-8
Nehemiya Anali Woyang’anira Wabwino
Tishiri 455 B.C.E.
N’kutheka kuti panthawiyi m’pamene Nehemiya anasonkhanitsa anthu kuti alambire Yehova
Anthu anasangalala kwambiri
Anthu amene anali mitu ya mabanja anasonkhana kuti aone zimene angachite kuti azitsatira kwambiri Chilamulo cha Mulungu
Anthu anakonzekera kuchita Chikondwerero cha Misasa