Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsamba 6
  • Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • KODI TINGASONYEZE BWANJI CHIKONDI . . .
  • Dikirani Yehova
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2006
  • Zokumbutsa za Msonkhano Wachigawo wa 1998 Wakuti: “Njira ya Moyo ya Mulungu.”
    Utumiki Wathu wa Ufumu—1998
  • Nthawi ya Chakudya Chauzimu Ndiponso Yosangalala
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2008
  • Masiku Atatu Otsitsimulidwa Mwauzimu
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 April tsamba 6

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo

Pa nthawi ya msonkhano wachigawo tikufunitsitsa kudzasonyeza anthu chikondi ngati mmene timachitira nthawi zonse. (Mateyu 22:37-39) Lemba la 1 Akorinto 13:4-8, limafotokoza zimene chikondi chimachita, limati: “Chikondi n’choleza mtima ndiponso n’chokoma mtima. . . . sichichita zosayenera, sichisamala zofuna zake zokha, sichikwiya. . . . Chikondi sichitha.” Mukamaonera vidiyo ya Zofunika Kukumbukira Pamsonkhano Wachigawo, muziganizira mmene mungadzasonyezere ena chikondi pa nthawi ya msonkhano.

KODI TINGASONYEZE BWANJI CHIKONDI . . .

  • tikamasunga malo okhala?

    Banja lakhala moyandikana pamsonkhano ndipo silinasiye mipando ina yopanda anthu
  • nyimbo zomvetsera zikatsala pang’ono kuyamba?

    A Mboni za Yehova akhala pansi ndipo akumvetsera nyimbo msonkhano usanayambe
  • kumalo ogona ngati tapeza malo kuhotelo kapenanso kwinakwake?

    Banja likufika ku hotelo
  • tikamadzipereka kugwira nawo ntchito zina?

    Malo amsonkhano
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena