CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 38-44
Yehova Amasamalira Anthu Omwe Akudwala
Anthu amene amatumikira Yehova mokhulupirika amamudalira pa mavuto aliwonse
Davide anadwala kwambiri
Davide ankathandiza anthu onyozeka
Davide sankayembekezera kuti achira mozizwitsa, koma anapempha Yehova kuti amupatse nzeru, amutonthoze ndiponso amuthandize
Yehova ankaona kuti Davide anali munthu wokhulupirika