CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 1-3
Kukhala Okhulupirika kwa Yehova Kumabweretsa Madalitso
Nkhani ya anyamata atatu Achiheberi ingatithandize kukhalabe okhulupirika kwa Yehova
Mogwirizana ndi malemba ali m’munsiwa, kodi kukhala okhulupirika kwa Yehova kumaphatikizapo chiyani?