CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 10-12
Yehova Ananeneratu Zokhudza Mafumu a Mtsogolo
Padzakhala mafumu 4 ochokera mu ufumu wa Perisiya. Mfumu ya nambala 4 “idzaukira ufumu wa Girisi ndi mphamvu zake zonse.”
Koresi Wamkulu
Kambisesi II
Dariyo I
Sasta I (ena amati ndi Mfumu Ahasiwero amene anakwatira Esitere)
Mfumu yamphamvu ya Girisi inayamba kulamulira dera lalikulu kwambiri.
Alekizanda Wamkulu
Akuluakulu 4 a asilikali a Alekizanda anagawana ufumu wa Girisi.
Kasanda
Lasamekasi
Selukasi I
Tolemi I