Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 December tsamba 2
  • Funafunani Yehova Tsiku la Mkwiyo Wake Lisanafike

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Funafunani Yehova Tsiku la Mkwiyo Wake Lisanafike
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Funafunani Yehova Lisanadze Tsiku la Mkwiyo Wake
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Tengerani Chitsanzo kwa Aneneri—Zefaniya
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2005
  • “Funani Yehova, Ofatsa Inu Nonse”
    Nsanja ya Olonda—1993
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 December tsamba 2
Zefaniya akulankhulana ndi Aisiraeli

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | ZEPHANIYA 1–HAGAI 2

Funafunani Yehova Tsiku la Mkwiyo Wake Lisanafike

Zef. 2:2, 3

Kuwonjezera pa kudzipereka kwa Yehova, pali zambiri zimene tiyenera kuchita kuti tidzapulumuke patsiku la mkwiyo wake. Tiyenera kumvera malangizo amene Zefaniya anapereka kwa Aisiraeli.

  • Bwerani kwa Yehova: Tipitirize kukonda Yehova komanso kugwirizana ndi gulu lake

  • Yesetsani kukhala olungama: Tizitsatira mfundo zolungama za Yehova

  • Yesetsani kukhala ofatsa: Tiyenera kumvera Mulungu modzichepetsa n’kumalola kuti azitilangiza

Kodi ndi zinthu zinanso ziti zimene ndingachite kuti ndizifunafuna Yehova, ndikhale wolungama komanso kuti ndikhale wofatsa

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena