CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MALAKI 1-4
Kodi Ukwati Wanu Umakondweretsa Yehova?
M’nthawi ya Malaki, anthu ambiri ankathetsa ukwati pa zifukwa zosamveka. Yehova sankavomereza kulambira kwa munthu amene wachitira zachinyengo mwamuna kapena mkazi wake
Yehova anadalitsa anthu amene ankalemekeza amuna kapena akazi awo
Kodi anthu okwatirana angasonyeze bwanji kuti ndi okhulupirika kwa mnzawo pa zimene . . .
amaganiza?
amayang’ana kapena kuonera?
amalankhula?