Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 February tsamba 2
  • Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Mverani Ndipo Mumvetse Tanthauzo Lake’
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Kuwala Kukuwonjezerekabe
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
  • Mafanizo Oyenerera
    Buku Lolangiza la Sukulu ya Utumiki Wateokalase
  • “Nthawi Zonse Iye Ankalankhula Nawo Pogwiritsa Ntchito Mafanizo”
    ‘Bwera Ukhale Wotsatira Wanga’
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 February tsamba 2

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mfundo Zimene Tingaphunzire Kuchokera M’mafanizo Onena za Ufumu

Yesu ankagwiritsa ntchito mafanizo osavuta kumva pophunzitsa mfundo zozama zachoonadi. Komabe, ndi anthu odzichepetsa okha amene ankamvetsa komanso kugwiritsa ntchito mfundo zomwe ankaphunzira m’mafanizowa. (Mat. 13:10-15) Pa mafanizo onena za Ufumu otsatirawa, yankhani mafunso awa: Kodi ndikuphunzira chiyani m’fanizoli? Kodi zimene ndikuphunzirazi ndingazigwiritse ntchito bwanji pa moyo wanga?

Kanjere ka mpiru, zofufumitsa, chuma, wamalonda woyendayenda

UFUMU WAKUMWAMBA ULI NGATI . . .

  • “kanjere ka mpiru.”​—Mat. 13:31, 32; w14 12/15 8 ¶9.

  • “zofufumitsa.”​—Mat. 13:33; w14 12/15 9-10 ¶14-15.

  • “chuma” ndi “wamalonda woyendayenda.”​—Mat. 13:44-46; w14 12/15 10 ¶18.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena