Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yb16 tsamba 25-tsamba 27 ndime 1
  • Kuwala Kukuwonjezerekabe

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuwala Kukuwonjezerekabe
  • Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Kodi Mukukumbukira?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • “Usadzachite Nawo Mgwirizano wa Ukwati”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
yb16 tsamba 25-tsamba 27 ndime 1
Antchito akugwira ntchito m’munda wa tirigu

ZIMENE ZACHITIKA M’CHAKA CHAPITACHI

Kuwala Kukuwonjezerekabe

AKHRISTU oona amadalira kwambiri Yehova chifukwa amadziwa kuti ndi amene amawathandiza kuti azimvetsa mfundo za m’Baibulo. Choncho, nthawi zonse amapemphera kwa Mulungu kuti ‘kuwala ndi choonadi chake’ ziziwatsogolera. (Sal. 43:3) Anthu ambiri m’dzikoli ali mumdima wandiweyani. Komabe, Yehova akuthandiza anthu ake kumvetsa mfundo zina zatsopano. Kumvetsa bwino mfundo zolondola kuli “ngati kuwala kwamphamvu kumene kumamka kuwonjezereka.” (Miy. 4:18) Yehova akuthandiza atumiki ake kuti aone kuwala kwakukulu posintha zinthu zina m’gulu lake, posintha mmene ankamvera mfundo zina komanso powathandiza kusintha makhalidwe awo. Ndiye kodi ndi mfundo ziti zomwe zafotokozedwanso mwatsopano zaka zapitazi?

2012

“Maufumu ena onsewo”—Dan. 2:44

w12 6/15 tsa. 17

Moredekai ndi Esitere ‘adzagawana zimene afunkha’—Gen. 49:27

w12 1/1 tsa. 29

“Mfumu ya maonekedwe oopsa” idzawononga zinthu—Dan. 8:23, 24

w12 6/15 tsa. 16

Tanthauzo la zala za fano lomwe Nebukadinezara analota—Dan. 2:41-43

w12 6/15 tsa. 16

Nthawi imene ulamuliro wa 7 unayamba kulamulira

w12 6/15 tsa. 15, 19

2013

“Kapolo wokhulupirika ndi wanzeru”—Mat. 24:45-47

w13 7/15 tsa. 8, 20-25

‘Kapolo woipa’—Mat. 24:48-51

w13 7/15 tsa. 24

Aramagedo ikamadzayamba, odzozedwa adzakhala atapita kumwamba

w13 7/15 tsa. 5

“Msuri akadzalowa m’dziko lathu”—Mika 5:5

w13 11/15 tsa. 20

Adzasonkhanitsa anthu osankhidwa—Mat. 24:31; Maliko 13:27

w13 7/15 tsa. 5

Chisautso chachikulu

w13 7/15 tsa. 3-8

Fanizo la tirigu ndi namsongole—Mat. 13:24-30

w13 7/15 tsa. 13-14

Kubwera komanso kufika kwa Yesu—Mat. chaputala 24 ndi 25

w13 7/15 tsa. 7-8, 24

Yesu anayendera kachisi wauzimu kuyambira mu 1914 mpaka 1919—Mal. 3:1-4

w13 7/15 tsa. 11-12

Tanthauzo la dzina la Yehova

Kabuku Kothandiza Kuphunzira tsa. 5

2014

Kuika paudindo akulu komanso atumiki othandiza

w14 11/15 tsa. 28-29

Chifukwa chake Ayuda “anali kuyembekezera” Mesiya—Luka 3:15

w14 2/15 tsa. 26-27; w14 6/15 tsa. 22

Kutalika kwa nthawi yomwe kachisi wauzimu anayeretsedwa—Mal. 3:1-4

w14 11/15 tsa. 30

Kodi anthu amene adzaukitsidwe azidzakwatira kapena kukwatiwa?—Luka 20:34-36

w14 8/15 tsa. 29-30

“Maziko olimba a Mulungu”— 2 Tim. 2:19

w14 7/15 tsa. 8-9, 13

Mboni ziwiri—Chiv. chaputala 11

w14 11/15 tsa. 30

2015

Gogi wa kudziko la Magogi—Ezek. chaputala 38 ndi 39

w15 5/15 tsa. 29-30

Kodi mlongo ayenera kuvala chinachake kumutu akamachititsa phunziro la Baibulo?

w15 2/15 tsa. 30

Fanizo la matalente—Mat. 25:14-30

w15 3/15 tsa. 20-24

Fanizo la anamwali 10—Mat. 25:1-13

w15 3/15 tsa. 13-16

Kafotokozedwe ka nkhani kosonyeza kuti zinthu zotchulidwa m’Baibulo zikuimira zinazake

w15 3/15 tsa. 9-11, 17-18; w15 6/15 tsa. 32

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena