CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yoswa.]
Muziphunzira komanso kugwiritsa ntchito Mawu a Mulungu (Yos 1:7, 8; w13 1/15 8 ¶7)
Muzidalira Yehova mukamachita zimene amafuna (Yos 1:9; w13 1/15 11 ¶20)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndi pa nthawi ziti pamene ndingafunike kuchita zinthu molimba mtima?’