Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsamba 6
  • Yehova Amadalitsa Anthu Achikhulupiriro

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yehova Amadalitsa Anthu Achikhulupiriro
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kuwala Kukuwonjezerekabe
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 September tsamba 6
Ansembe anyamula likasa la pangano ndipo akuponda madzi a mu mtsinje wa Yorodano amene akuthamanga kwambiri.

Ansembe anyamula Likasa ndipo akuwoloka mtsinje wa Yorodano

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amadalitsa Anthu Achikhulupiriro

Malangizo a Yehova akhoza kuoneka ngati osathandiza potengera mmene anthufe timaonera zinthu (Yos 3:12, 13; it-2 105; onani chithunzi chapachikuto)

Anthu amene ali ndi udindo ayenera kukhala zitsanzo zabwino potsatira malangizo (Yos 3:14; w13 9/15 16 ¶17)

Yehova amadalitsa anthu amene amachita zinthu mosazengereza komanso molimba mtima (Yos 3:15-17; w13 9/15 16 ¶18)

Ansembe anyamula likasa la pangano pamene akuwoloka mtsinje wa Yorodano uli wouma.

Yehova amatidalitsa tikamayesetsa kulalikira ngakhale pamene sitingathe kuchita zambiri chifukwa cha thanzi lathu kapena mavuto ena.

Mlongo akulalikira kwa mzimayi wina atakhala pabenchi kupaki m’dziko limene ntchito yathu ndi yoletsedwa ndipo wapolisi akuyenda chapafupi.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena