Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 2
  • Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Mungachite Kuti Zinthu Zizikuyenderani Bwino
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amadalitsa Anthu Achikhulupiriro
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Mukutsanzira Mulungu Wathu Wopanda Tsankhu?
    Nsanja ya Olonda—1996
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 2
Ana aakazi 5 a Tselofekadi ali pakhomo la chihema chokumanako kuchonderera Mose kuti awathandize pa vuto lawo.

Ana aakazi 5 a Tselofekadi ankafuna kulandira cholowa cha bambo awo

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera

Ana aakazi 5 a Tselofekadi ankafuna kulandira cholowa cha bambo awo. (Nu 27:1-4; w13 6/15 10 ¶14; onani chithunzi chapachikuto)

Yehova anachita zinthu mosakondera (Nu 27:5-7; w13 6/15 11 ¶15)

Nafenso tiyenera kuchita zinthu mosakondera (Nu 27:8-11; w13 6/15 11 ¶16)

Timatsanzira Yehova yemwe ndi wosakondera tikamachita zinthu ndi Akhristu anzathu mwaulemu, tikamawasonyeza chikondi chokhulupirika, komanso tikamalalikira kwa anthu a mitundu yonse.

Mmene tingasonyezere kuti ndife osakondera. 1. Anthu 5 a misinkhu komanso mitundu yosiyana akucheza komanso kudyera pamodzi. 2. Banja likulalikira kwa munthu wosiyana naye mtundu pafupi ndi malo okhala anthu othawa kwawo.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena