Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsamba 4
  • Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • “Ndinetu Kapolo wa Yehova!”
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Kodi Nkhani ya Mariya Imatiphunzitsa Chiyani?
    Nsanja ya Olonda—2009
  • “Ndinetu Mdzakazi wa Yehova!”
    Nsanja ya Olonda—2008
  • ‘Anaganizira Tanthauzo la Mawu Onsewo Mumtima Mwake’
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 June tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 1

Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa

Yehova anasankha Mariya n’kumupatsa ntchito yapadera chifukwa anali ndi mtima wabwino.

Mngelo Gabrieli akulankhula ndi Mariya

1:38, 46-55

Kodi zimene Mariya analankhula zimasonyeza bwanji kuti . . .

  • anali wodzichepetsa?

  • anali ndi chikhulupiriro cholimba?

  • ankadziwa bwino Malemba?

  • anali ndi mtima woyamikira?

MAFUNSO OFUNIKA KUWAGANIZIRA:

Kodi ndimakhulupirira ndi mtima wonse kuti Yehova angandithandize pa china chilichonse mogwirizana ndi chifuniro chake? Kodi ndingatsanzire bwanji Mariya?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena