CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 21-22
“Chipulumutso Chanu Chikuyandikira”
Posachedwapa Yesu abwera kudzawononga oipa ndi kupulumutsa anthu okhulupirika. Tiyenera kukhala okonzeka kuti tidzapulumuke.
Palibe Vidiyo.
Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.