CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 1-2
Chozizwitsa Choyamba cha Yesu
Chozizwitsa choyamba chimene Yesu anachita chimatithandiza kumudziwa bwino. Kodi mavesiwa akusonyeza bwanji kuti Yesu anali ndi makhalidwe otsatirawa?
Ankaona moyenera zosangalatsa komanso ankapeza nthawi yocheza ndi anzake
Ankaganizira mmene anthu ena akumvera
Anali wowolowa manja