Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 September tsamba 5
  • Sipanawonongeke Chilichonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Sipanawonongeke Chilichonse
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Muzigwira Ntchito Yanu Mwaluso
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Gwiritsani Ntchito Mwanzeru Mabuku Athu Ofotokoza Baibulo
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
  • Kodi Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwanji ku Warwick?
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
  • Kodi Mumayamikira Mabuku Athu?
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2000
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 September tsamba 5
Likulu la dziko lonse ku Warwick, New York

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Sipanawonongeke Chilichonse

Yesu atadyetsa mozizwitsa amuna oposa 5,000 kuphatikizapo akazi ndi ana, anauza ophunzira ake kuti: “Sonkhanitsani zotsala zonse, kuti pasawonongeke chilichonse.” (Yoh. 6:12) Yesu anasonyeza kuyamikira zimene Yehova anam’patsa, popewa kuwononga zinthu.

Masiku anonso, Bungwe Lolamulira limayesetsa kutsanzira Yesu pogwiritsa ntchito mosamala zinthu zimene abale ndi alongo amapereka. Mwachitsanzo, pomanga likulu lathu la padziko lonse, m’tawuni ya Warwick ku New York, abale anasankha pulani yabwino n’cholinga choti pasamadzaonongeke ndalama zambiri.

KODI TINGAPEWE BWANJI KUWONONGA ZINTHU . . .

  • M’bale akuthimitsa magetsi pa Nyumba ya Ufumu

    tikakhala pamisonkhano yachikhristu?

  • Wa Mboni za Yehova akulemba dzina lake m’Baibulo lake

    tikamatenga mabuku oti tizigwiritsa ntchito ifeyo? (km 5/09 3 ¶4)

  • M’bale akutenga timapepala tomwe akuona kuti tingamukwanire

    tikamatenga mabuku oti tizigwiritsa ntchito tikamalalikira? (mwb17.02 “Tizigwiritsa Ntchito Mwanzeru Mabuku Ndiponso Magazini” ¶1)

  • Mlongo akuonetsetsa kaye ngati mwininyumba ali ndi chidwi asanamugawire chilichonse

    tikakhala mu utumiki? (mwb17.02 4 ¶2, ndi bokosi)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena