Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 July tsamba 3
  • “Pitirizani Kutonthozana ndi Kulimbikitsana”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Pitirizani Kutonthozana ndi Kulimbikitsana”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Tipitirize Kulimbikitsana Tsiku ndi Tsiku
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Tizilimbikitsana Ndipo “Tiwonjezere Kuchita Zimenezi”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Tizilimbikitsana
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Tizilimbikitsana
    Imbirani Yehova
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 July tsamba 3
Mlongo wachikulire akuthirira khofi alongo awiri achitsikana

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 ATESALONIKA 1-5

“Pitirizani Kutonthozana ndi Kulimbikitsana”

5:11-14

Mkhristu aliyense akhoza kulimbikitsa ena. Mwachitsanzo, timalimbikitsa Akhristu anzathu ngati nthawi zonse timapezeka pamisonkhano komanso kulalikira. Tingawalimbikitse ngakhale zitakhala kuti tikuchita zimenezi “movutikira kwambiri” chifukwa cha matenda kapena mavuto ena. (1 Ates. 2:2) Komanso tikamaganizira zimene tinganene, mwinanso kufufuza mfundo zina m’mabuku athu, tikhoza kumatonthoza ndiponso kulimbikitsa abale athu.

Kodi mungapeze kuti mfundo zimene mungagwiritse ntchito polimbikitsa munthu amene ali ndi vuto linalake?

Kodi ndi ndani mumpingo wanu amene mukufuna kumulimbikitsa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena