Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 December tsamba 5
  • Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Adzatsogolera Anthu ku Mtendere Ndani?
    Nsanja ya Olonda​—1990
  • Mtendere Weniweni—Kodi Udzachokera Kuti?
    Nsanja ya Olonda—1997
  • Kodi Nliti Pamene Mtendere Wokhalitsa Udzabweradi?
    Nsanja ya Olonda—1991
  • Aramagedo Nkhondo ya Mulungu Yothetsa Nkhondo Zonse
    Nsanja ya Olonda—2008
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 December tsamba 5
Yesu ali pahatchi ndipo mkamwa mwake mwatuluka lupanga lalitali, kumbuyo kwake kukubwera gulu lankhondo lomwe okwerapo ake avala zoyera

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 17-19

Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse

19:11, 14-16, 19-21

N’chifukwa chiyani Yehova, yemwe ndi “Mulungu wachikondi ndi wamtendere” anauza Mwana wake yemwe ndi “Kalonga Wamtendere” kuti adzamenye nkhondo?​—2 Akor. 13:11; Yes. 9:6.

  • Yehova ndi Yesu amakonda chilungamo ndipo amadana ndi zoipa

  • Mtendere weniweni ndi chilungamo zidzakhalapo anthu oipa akadzawonongedwa

  • Gulu lankhondo la Mulungu ‘lidzamenya nkhondo mwachilungamo,’ ndipo zimenezi zikuonekera chifukwa omenya nkhondowo akwera mahatchi oyera komanso avala zovala zoyera

Kodi tingatani kuti tidzapulumuke pa nkhondo yofunikayi?​—Zef. 2:3

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena