Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsamba 2
  • ‘Mulungu Anayesa Abulahamu’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Mulungu Anayesa Abulahamu’
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Umboni Waukulu Wakuti Mulungu Amatikonda
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Kodi N’chifukwa Chiyani Mulungu Anauza Abulahamu Kuti Apereke Mwana Wake Nsembe?
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Abulahamu Anasonyeza Kuti Anali Wokhulupirika
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Mulungu Ayesa Abrahamu
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 March tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 22-23

‘Mulungu Anayesa Abulahamu’

22:1, 2, 9-12, 15-18

Abulahamu anamva chisoni kwambiri pamene ankafuna kupereka nsembe mwana wake Isaki. Zimenezi zimatithandiza kumvetsa mmene Yehova anamvera pamene ankapereka mwana wake Yesu Khristu monga dipo. (Yoh 3:16) Kodi mawu amene Yehova ananena muvesi 2 akutithandiza bwanji kudziwa mmene amamvera?

1. Abulahamu wagwira mpeni m’manja mwake ndipo akuyang’ana kumwamba pamene Isaki wagona pa guwa lansembe. 2. Yesu wapachikidwa pamtengo.

Kodi mumamva bwanji mukaganizira chikondi chimene Yehova ali nacho?​—1Ak 6:20; 1Yo 4:11

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena