Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 July tsamba 2
  • “Tsopano Uona Zimene Ndichite kwa Farao”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Tsopano Uona Zimene Ndichite kwa Farao”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Yehova Ndani?
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Mfumu Yoipa Ilamula Igupto
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • ‘Yehova Wakhala Chipulumutso Changa’
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Kuoloka Nyanja Yofiira
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 July tsamba 2
Aisiraeli ndi anthu ena omwe si Aisiraeli akutuluka mu Iguputo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 6-7

“Tsopano Uona Zimene Ndichite kwa Farao”

6:1, 6, 7; 7:4, 5

Asanabweretse miliri ku Iguputo kuti atulutse Aisiraeli ku ukapolo, Yehova anauziratu Aisiraeliwo zimene ankafuna kuchita. Iwo adzaona Yehova akusonyeza mphamvu zake m’njira imene anali asanaionepo, ndipo zimenezi zidzachititsa Aiguputo kudziwa kuti Yehova ndi ndani. Mulungu atakwaniritsa zomwe analonjeza, chikhulupiriro cha Aisiraeli chinalimba ndipo zimenezi zinawathandiza kuti asatengere kulambira konyenga kwa Aiguputo.

Kodi nkhani imeneyi yakuthandizani bwanji kulimbitsa chikhulupiriro chanu kuti malonjezo onse amene Mulungu ananena adzakwaniritsidwa?

Atumiki okhulupirika a Yehova akutuluka mu chisautso chachikulu.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena