Mose watambasula dzanja lake kuti alekanitse madzi pa Nyanja Yofiira
Zimene Tinganene
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti mfundo zimene zingatithandize tikaferedwa?
Lemba: 2Ak 1:3, 4
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?
○● ULENDO WOBWEREZA
Funso: Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi anthu amene anamwalira angadzakhalenso ndi moyo?