Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 August tsamba 2
  • “Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • B5 Chihema Chopatulika Komanso Mkulu wa Ansembe
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yehova Ndi Wamphamvuyonse Koma Amaganizira Ena
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • “Chirimikani, Ndipo Penyani Chipulumutso cha Yehova”
    Nsanja ya Olonda—2007
  • “Ndakupatsani Chitsanzo”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 August tsamba 2
Aisiraeli akuwoloka Nyanja Yofiira panthaka youma. Kuwala kwa moto woima njo ngati chipilala kukuunikira njira yawo.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 13-14

“Chilimikani ndi Kuona Chipulumutso cha Yehova”

14:13, 14, 21, 22, 26-28

Yehova ndi Mpulumutsi amene amaganizira anthu ake. Kodi anasonyeza bwanji kuti ankaganizira kwambiri Aisiraeli pamene ankachoka ku Iguputo?

  • Anawathandiza kuyenda mwadongosolo.—Eks 13:18

  • Ankawatsogolera komanso kuwateteza.—Eks 14:19, 20

  • Anapulumutsa anthu ake onse, kuyambira ana mpaka achikulire.​—Eks 14:29, 30

Kodi sitiyenera kukayikira za chiyani pamene chisautso chachikulu chikuyandikira?​—Yes 30:15

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena