Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 December tsamba 5
  • Timafunika Kukhala Oyera Kuti Tizilambira Mulungu Movomerezeka

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Timafunika Kukhala Oyera Kuti Tizilambira Mulungu Movomerezeka
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Anatiyeretsa Kuti Tichite Ntchito Zokoma
    Nsanja ya Olonda—2002
  • Mulungu Amakonda Anthu Oyera
    Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
  • Kodi Mukukhalabe Osadetsedwa m’Njira Iriyonse?
    Nsanja ya Olonda—1987
  • Atumiki a Mulungu Ayenera Kukhala Oyera
    Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife?
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 December tsamba 5

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 14-15

Timafunika Kukhala Oyera Kuti Tizilambira Mulungu Movomerezeka

15:13-15, 28-31

Kuti Mulungu azitikonda, tiyenera kukhala aukhondo komanso zochita ndi zoganiza zathu ziyenera kukhala zoyera. Zimenezi zikutanthauza kuti tiyenera kutsatira mokhulupirika mfundo za Yehova zokhudza ukhondo, makhalidwe komanso kumulambira. Tiyenera kuzitsatira ngakhale kuti anthu am’dzikoli sachita zimenezi. Tiyeneranso kupewa kuchita chilichonse chimene Atate wathu wakumwamba amaona kuti ndi chodetsedwa.

Zithunzi zosonyeza zinthu zoipa zam’dzikoli. 1. M’busa akupempherera asilikali. 2. M’busa wamkazi akudalitsa ukwati wa amuna okhaokha. 3. Chithunzi chosonyeza kubadwa kwa Yesu komanso mtengo wa Khirisimasi zomwe zili mushopu yayikulu.

Kodi kupewa zinthu zoipa zam’dzikoli kumandithandiza bwanji?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena